Stonecroft
Stonecroft Training
Mndandanda wa Utatu
Malangizo Otsogolera
Mavesi a m'Baibulo
Adult Stonecroft International
The International Team
English YDT Teachings
Maphunziro a Ana
Malawi Moringa Projects
|
|
home >>stonecroft>>
yesu ndani? >>phunziro 5 >>phunziro 6
Stonecroft - YESU NDI NDANI?- Phunziro #6
Ndidzamuona Yesu?
Pemphero
Wokondedwa Atate ku mwamba, Zikomo potiphunzitsa zambiri za chimene
Yesu ali.
Tiphunzitseni tidziwe za mbiri kuchokera mu Buku Lanu pamene tikuphunzira
phunzirori.
Tikufuna tidziwe ngati tidzamuonadi Yesu. Mu dzina lache, ame.
Kuwerenga Baibulo kwa Sabata:
Werengani gawo la baibulo pansipa ndipo mulembe fundo ya tanthauzo
logwira
ntima limene malimva pa kuwerengedwa kulikonse.
Yohane 1:14-18
Yohane 14:1-11
1 Yohane 5:10-12
Mateyu 16:24-27
Afilipi 2:5-11
1 Atesolonika 4:15-18
Yohane 5:24-29
|
1 a. Yesu ndi ndani kwa inu? . . . . . |
b. Kodi Yesu anati lamulo lofunikira kwambiri
ndi liti? Mateyu 22:36-40
|
c. Yesu anachita zinthu zambiri zofunika akanali
pa dziko lapansi. Ntchito yofunikira
kwa mbiri ndi chifukwa chimene anabwerera. Chimnali chani?
Marko 10:45
|
2. Lembani mu magawo awa. sankhani ku mau awa:
mlowa malo |
fuko |
chosatheka |
kufa thupi |
losachima |
kubadwa |
mwa |
namwali |
makumi |
anayi |
Mulungu |
kuikidwa |
m'manda |
kulipira |
kulamulira |
chikhululukiro |
umuyaya |
chitatu |
mtanda |
mwana |
wa nkhosa |
tchimo |
|
|
Dipo ........................ analilamula kuti lichitike
pa pa anthu ochimwa inali ................... Nthawi
isanayambe, Mulungu anati osalakwa ..................................kufa
m'malo a munthu
ochimwa.Anthu amapereka sembe ya nyama yopanda banga—makamaka
....................—akafuna Mulungu kuwakhululukira
machimo awo. Mwazi wa nkhosa
umene anaupereka sunachots ..........................
Inali chifanizo cha nsembe yoyera imene
Mulungu anayitumiza. Imaphimba tchimo lawo, kufikira Yesu kubwera
pa dziko
............................. chifukwa cha machimo a dziko lapansi.
Koma kufa, Amayenera kukhala ndi thupi la munthu ................,
chifukwa anali
Mulungu, ndipo kunali ............................
kuti Mulungu afe. Chifukwa chache, anasankha
ndi kukonzekeretsa .................. limene anakonzekeretsa
thupi la Iye. ............................ iwo
ku ..........................a dziko lapansi ndikuwapatsa
malamulo kuti atsate a kukhala mwa
.........................
Nthawi itakwana, malingana ndi dongosolo Lache, anabwera ku
Dziko ngati
Myuda, ..............................................
mwana. Anakhala m'moyo ...........................
.............................................................
koma pa tskiku ........................Anawuka kwa
akufa,
kudzionetsera Yekha anali wa moyo. ataonedwa ndi anthu ambiri
kwa masiku
makumi anayi, Anakwera ku mwamba.
Ngongol ..................................younse.
Mbali yathu ndi kulandira ....................................
cha
Mulungu ndi mphatso ya moyo .....................
Ichi chitanthauza tikulandira imfa ya
Yesu pa mtanda ngati dipo la matchimo athu. Timalola This
means that we accept
Jesus Christ’s death on the cross as payment for our
personal sin debt. Timalola
Mulungu .........................miyoyo yathu. |
Kodi chifukwa chani ndikofunika kuti wina aliyense adziwe zinthu
izi? ndizofunika chifukwa chikhulupiriro chmapanga chikhalidwe.
Chimene timakhulupirira chimapanga chimene timachita ndi m'mene
timachitira. Chifukwa chake ndikofunika kukhala ndi kumvetsetsa
kwa bwino za chimene Yesu ali.
Chikhulupiriro
chimaumba Chikhalidwe.
|
3. Yesus akabwera msogolo, adzamuone ndani? Chibvumbulutso
1:7 |
4.Baibulo limati kudzakhala nthawi ya masautso ndi chizunzo
pa dziko la pansi.
Werengani zimene zidzachitike pa dziko Yesu asanabwerenso,
ndipo mulembe
zimene zakupatsani chidwi powerenga izi.
a. Mateyu 24:21-31
b. Marko 13:32-37
c. Luka 21:25-28, 34-36 |
5. Kodi chimachitika n'chiyani munthu akamwalira?
Ahebri 9:27
|
6. a. 2 Akorinto 5:10
b. Machitidwe 17:30-31
c. Chibvumbulutso 20:11-15
Anthu akamakamba za kupulumutsidwa, amakamba za kupulumutsidwa
ku chilango chosatha mu nyanja ya moto.
Tikamawerenga za chimene Mulungu amanena za chiwerezo chache
cha chilungamo, timazindikira kuti kulandira Yesu kumatipulumutsa
ife kuchilango chotiyenera. Tikuyenera kukhala ofuna kudzipereka
mwathunthu kwa Iye. Mitima yathu ikhale yodzala ndi matamando
kwa Iye pa chipulumutso chake chachikulu!
|
Mulungu safuna alo munthu m'modzi apite ku gahena.
Iye anapangira gahena
kukhala ya satana ndi amithenga ake.—osati anthun (Mateyu
25:41). Anthu ali
omasuka kusankha Mulungu kapena satana.
|
Khalani mukudziwa za Umuyaya!
7 a.Kozi zimene maphunzira zikupindura chani pa moyo wanu
wa tsiku ndi tsiku?
2 Akorinto 7:1
b. Kodi maonedwe anu pa zakukhala ndi zinthu ndi zimene mukulingalira
mutatenga ndi kukhala nazo asintha motani? Mateyu
6:19-21
c.Kodi zoti Mzimu Woyera akukhala mwa okhulupirira zimathawathandizira
bwanji m'maonedwe awo pa za ziphinjo ndi zokhumudwitsa?
Yakobo 1:2-4
d. Kodi chidziwitso cha dongosolo la Mulungu chikuyenera
kuchita chani pa maonedwe a okhulupirira pa za kugawa uthenga
wabwino kwa wena. 2 Timothy 4:1-5
e. Kodi 1 Akorinto 15:58, amalimbikitsa
bwanji okhulupirira kuti akhale wamachawi mu ntchito ya Mulungu? |
8. Maphunziro a Mau a Mulungu amasintha miyoyo.
Maphunziro awa akusinthani
bwanji myo wanu? |
9. Lembani pemphero kufotokozera mathokozo anu kwa Mulungu potumiza Mwana
Wake, Yesu Khristu. Pazokambirana, mudzakhala ndi kusankha
kogawa pemphero
lanu. Lembani pempher lanu apa.
|
Pemphero Lotsekera
Tate wathu wakumwamba, zikomo chifukwa chobwera pa dziko kudzatifera,
zikomo chifukwa chobwera pa dziko mkudzadzitengera chilango machimo
athu. Zikomo polola kukhala m'moyo wathu. Zikomo chifukwa cha lonjezo
simudzatisiya tokha! Tithandizeni kupereka miyoyo yathu kuti uilamulire.
Malizani zimene mayamba m'moyo wa wina aliyense. Tapemphera mu dzina
la Yesu, Ameni.
|
|