Project Hope     home >>stonecroft>> yesu ndani? >>phunziro 1 >>phunziro 2
Stonecroft - YESU NDI NDANI?- Phunziro #2
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

Yesu anati chani?

Pemphero

Atate wokondedwa wa kumwamba, Buku ilo munalemba ndi lamphamvu! Ndilodzala ndi
choonadi! Tikufuna tiphunzire zimene Yesu adaphunzitsa anthu. Tsegulani maso athu kuti kuti tione ndi kumvetsa mau Ake. Tapemphera mu dzina Lake lodabwitsa, ame

Kuwerenga Baibulo kwa Sabata:

Mateyu 5:1-12

Mateyu 5:13-16

Mateyu 6:1-15

Mateyu 6:24-34

Mateyu 7:1-12

Mateyu 7:13-20

Mateyu 7:21-27

1. Mulungu anadzivumbulutsa Yekha kwa mose ngati InGod introduced Himself to
Moses as INE NDINE AMENE NDIRI (Exodo 3:14). Kawiiri mu Uthenga Wabwino,
Yesu akudzichula kuti NDINE. Akumaliza ziganizo zimene zikuonka zosamaliza.
(NDINE…) ndi mau amene amafotokoza za chimene ali kwa iwo omukhulupirira Iye.)

Werengani ziganizozi ndipo mumalize.

a. Yohane 13:19. . . . . Ndine ........................................................................................................

b. Yohane 8:12. . . . .. Ndine ........................................................................................................

c. Yohane 10:9. . . . .. Ndine ........................................................................................................

d. Yohane 10:11. . . . Ndine ........................................................................................................

e. Yohane 10:36. . . . Ndine ........................................................................................................

f. Yohane 11:25. . . . Ndine ........................................................................................................

g. Yohane 6:48. . . . . Ndine ........................................................................................................

h. Yohane 14:6. . . . . Ndine ........................................................................................................

Maina operekedwa kwa Yesu mu phunziro 1 ndi funso lapambuyo akuonetsera
chikhalidwe Chake.

Pa mthawi zosiya m'miyoyo yathu, maina ena aYesu ndi athanthauzo lomvekabwino
kwa ife. Mwachitsanzo, pa nthawi imene tikufuna chitetezo ndi citsogozo, dzina,
"Mbusa wa Bwino" litha kukhala la tanthauzo lalikulu kwa ife. Pamene tikuwerenga
Baibulo ndi kumadya chakudya cha uzimu, ndi "Mkate wa Moyo" wathu.

2. Ndi dzina liti limene lili ndi tanthauzo pa nyengo mukudutsa pano.. . . . .


"Chiphunzitso cha pa Phiri"

Chiphunzitso chimene Yesu analalikira Chiphunzitso ndi “Malankhulidwe opereka malangizo mu chipembedzo kapena chikhalidwe”

3. Werengani Chiphunzitso cha pa Phiri chodziwika bwino chimene chikupezeka pa, Mateyu 5:1-7:29. Lembani mitu ndi za Mbaibulo zili pansinzi zimene zili zopindulitsa kwa inu.

Chitsanzo:
Kuphunzitsa za kukwiya. . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . . ..... .. . . Mateyu 5:21-26

 

Fanizo lomwe Yesu ananena

Fanizo ndi kankhani kakafupikamene kamafotokoza za uzimu ndi chikhalidwe


4. Patsiku lina. pambali pa mtsinje, Yesu analalikira chiphunzitso cha mphamvu
chimene chili ndi mafanizo asanu ndi awiri. Tsekulani tsamba 34-38 ndipo werengani
ulalikiwu—Mateyu 13:1-58. Werengani maina a mafanizo asanu ndi mu gawo ili:

..................................................................................................................................................................

Ananenera za Iye, pamodzi, Yesu ananena mafanizo 60 amene analembedwa mu Uthenga Wabwino. Ena amabwerezedwa mu mauthenga ena abwino. Imodzi yodziwika bwino ndi fanizo la Ofesa.

5. Mateyu, Marko, and Luka ikunena za matambasulidwe a Yesu pa fanizoli.
Werengani Luka 8:11-15 . . . . .

a. Kodi wofesa amadzala chani? . . . . .

b. Chimene chimalepheretsa ? . . . . .

c. Chifukwa chani nthaka ina imapindura kusiyana ndi yina?. . . . .


6. Lingalirani za fanizo lanthaka.

a. Ndi nthaka yanji imene moyo wanu ukuyimira?. . . . . (Mafunso asiyana.)

b. Ndi kusintha kwa ntundu wanji komwe kukufunika kuti moyo wanu usinthe
ndikukhala nthaka ya bwino.. . . . (Mafunso asiyana.)

Tsopano tiona ma uneneri ena a Yesu.

Mauneneri amene Yesu ananeneratu

Uneneri umachokera "pakuyankhula motsogozedwa ndi Mulungu"

7. Chipangano cha Tspopano chili ndi ma ulosi ambiri a Yesu. Ochepa ndi awa ali
pansipa. Lembani fundo ya Baibulo yolondola.

Marko 8:38
Marko14:72
Luka 24:5-7
Yohane 5:25-29
Yohane 12:32-33

Za m'Baibulo

a. Kukanidadwa ndi ophunzira ................................
b. Imfa yake...............................................................
c. Chiukitso Chake..................................................
d. Chiukitso chathu ..................................................
e. Kubweranso kwake ............................................

8. Mau amene Yesu amayankhula amachoka kuti?
Yohane 17:5-8 . . . . .
Mu chipangano cha Kale timawerenga nthawi zimene Mulungu analankhula kwa
aneneri, asembe, ndi mafumu. Baibulo linalemba izi kunena " Baibulo linanena izi kuti
"Mulungu anati......kapena Mau a Mbuye anabwera........" Mulungu analankhulanso
kwa anthu mu chipangano chatsopano.

9. Kwa ndani kumene Mulungu anapereka mau Ake ndi uthenga mu Chipangano cha
Tsopano munsimu?

a. Marko 1:10-11. . . . .
b. Yohane 1:32-33 . . . . .
c. Machitidwe 11:4-9 . . . . .

10. Mwaphunzira chani za Yesu ndi zimene anachita. . . . .

Pemphero lotsekera

Ambuye Yesu, zikomo tikudziwa zonse zimene munanena ndi zoona. Palibe analankhula ngati Munalankhulira. Titha kudalira malonjezano Anu. Zikomo potiphunzitsa. Tapemphera mu dzina Lanu, ame.

 
 

 

YESU NDI NDANI?

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us