home >>stonecroft>> ndondomeko yolondolera >>nthawi
yoyandikira ziphunzitso za baibulo
NTHAWI YOYANDIKIRA ZIPHUNZITSO
ZA BAIBULO.
NTHAWI YOYANDIKIRA ZIPHUNZITSO ZA BAIBULO.
Zofunikira zina zochepa:
Uyenera kubvomelezedwa ngati wolondolera wa Stonecroft momaliza
folomu yofunsira ya ziphunzitso za Baibulo za Stonecroft yomwe yatanthauzilidwa
muchilankhulo cha chiswahili kwa ofunsila a Tanzania.
Tikufuna kudziwa udindo wanu ndi mbali yanu pa mpingo.
Tikufuna kudziwa ngati mwawerenga mfund za zautumiki wa Stonecroft
ndi mfundo yachikhulupiliro kuti palibe chomwe mwakhuzidwa nacho
ZOFUNIKIRA PA ZIPHUNZITSO
1. Bukhu la chiyambi utatu woyera lophunzilira lotanthauzilliqwa
mu chiswahiri litha kupezeka kuchoka ku likulu la (ATBS) Mbeya,
Tanzania.
2. Mabukhu ophunzilira atha kutengedwa kuchoka ku Mbeya, Tanzania.
3. Baibulo la chiswahiri mgwirizano litha kupezeka kuchoka ku bungwe
la mabaibulo la Tanzania.
4. Kodi mungazikhulyupilire izi? Latanthauzilidwa mu chiswahili
ndipo litha kupezeka ku likulu lawo la (ATBS) ku Mbeya, Tanzania.
5. Makhadi a chidziwitso atanthauzilidwanso ndipo atha kupezeka
ku likulu lawo la (ATBS) ku Mbeya, Tanzania.
6. Fomu ya wolumikiza (wolondolera) lofunsira za uphunzitsi wa baibulo
titha kupezeka ku likulu la (ATBS) ku Mbeya, Tanzania.
Mupeze mala oyenelera a ziphunzitso zamubaibulo, muganizile zohita
maphunziro mnyumba, tchalitchi, mkalasi pa tsiku loweluka, mwina
panja pa mthunzi wabwino pansi pa mtengo.
KUKHONZEKERA ZIPHUNZITSO
Mumalizitse ziphunzitso polemba mayankho mu bukhu lophunzitsira
musanawerenge bukhu la ndondomeko. Izi zikuthandizani kumvetsetsa
malingaliro omwe ena atadutsemo kukafikira mayankho oyenelera
Muphunzire kuwerenga ziphunsitso mokweza ngati kungakhale koyenelera.
Musindikize malembo ofunikira ndi mau ena apadera omwe angakuthandizeni
kumvetsa bwino lanu kugulu.
• Under normal circumstances lessons
should not exceed 1 – 1 1/2 hours particularly if the Bible
Study is part of the Africa Women’s Empowerment Program (AWEP)
because the ladies will have to leave and start their Vocational
Training Lessons.
• At the same time as AWEP students are enjoying their Bible
Study their child will be attending their PowerClub to be trained
in the ways of God through Africa Bureau of Children’s Discipleship
Curriculum including the Grow and Go curriculum alongside the Drop of Hope Organic Kitchen Garden project as well as the 'Kids in Ministry International' curriculum and other children’s
ministry including Kids Evangelism and Youth Discipleship Programs.
• Initially the locations will be:
Tanzania – Africa Training Bible School (ATBS) – Mbeya
Tanzania (Swahili)
Uganda – Hope Community Centre, Kampala (English)
Malawi – Africa Training Bible School (ATBS) – Uluwa
and Vulwa, Malawi (Chichewi)
DR Congo - Africa Training Bible School (ATBS) (French)
NTHAWI YA ZIPHUNZITSO
Nthawi zonse yambani maphunziro ndi pemphero, ngati wina wake wanena
pempher, muganizile kuti gulu lilembe pa zopemphelerapo pa tsamba
la bukhu lophunzilira kumapeto ngati chikumbutso kudzapemphelerapo
mkati mwa sabata.
Ngati pempho ndilofunika msanga, muziikepo kuyamba kwa ziphunzitso
mupemphero lotsegulira.
Mukumbukire kuti pachiyambi pa phunziro la gawo lirilonse monga
yesu ndiye ndani? Munthu yense ayenera kulemba mayankho ake mubukhu
lophunzilira pa phunziro loyambilira. Pazotsatira zina zophunzilira
mulimbikitse gulu kumaliza maphunziro pakuyamba kwakukumanako potsindikiza
mayankho mubukhu lophunzilira musanafike kukalasi.
Muerenge ndikupeleka uthenga mubukhu lolondoza ndondomeko mwapamwamba
moyang’ana maso bwino lomwe kwa ophunzira. Wolondolera akuphunzira
nawo limodzi ndi gulu kuli oyenera kukhala kadaulo pa baibulo.
Wolondolola amayi kumveka bwino ndi mulingo wa ziphunzitso potsatira
izi:-
• Kuyamba ndikutsinzina panthawi yake, kumbukirani zambiri
za ziphunzitso zizikhala zophatikizana ndi ndondomeko ya amayi kupatsidwa
mphamvu ya Sstonecroft, ndiye, azimayi ayenera kuchoka ndikupita
kuziphunzitso zantchito yamanja pamapeto pake.
• Gwiritsani ntchito bukhu lolondoza ndondomeko ndi baibulo
lwa chiswahiri mgwirizano ndi ena mwa ma baibulo oyenera omasulidwa
bwino ku maiko ena, sipafunikanso zipangizo zina za padera..
• Limbikitsani wina aliyense kutenga nawo mbali muzokambirana,
kusalora kuti wina akulamulira kwambiri, muyenera kukhala okoma
mtimapomwe mukulibikitsa ena kutenga nawo mbali posamukhumudwitsa
yemwe akutenga nawo mmbali kwambiri.
Muyike maso pakuphunzira za yesu, osati osati ziphunzitso zawamba,
za ndale kapena zochitika mdera, mafunso aziphunzitso za wamba amatha
kutengedwa bwino panthawi inayoyenera bwino.
Nthawi zones yang’anani omwe ali mgulu omwe angadzakhale
olondolera ziphunzitso za mtsogjolo.
Ngati wolondolera mukhale chitsanzo choawonetsa tsankho. Muletse
anthu kuleka kukambirana zinthu zimene siziyenera kukambidwa pa
gulupo monga mikangano ya kunyumba kuwonjezera pa zochit za pa gulupo.
Mupemphere ndi anthuwo ndikuwalimbikitsa kufuna chitsogozo cha Mulungu.
Pomaliza pa dondosolo la azimayi kulandira mphamvu a Stonecraft,
aliyense amene angachite kulondolera bwino asankhidwe ndikuphunzitsidwa
kupeleka mwayi kwa omwe amaliza maphunziro kubwelera kumanyumba
kwawo potenganso ndi ziphunzitso zawo kumadera kwawoko.
Mufunse otenga nawo mbali za omwe angawaitane kumaphunziro ena
baibulo. Muwalimbikitse kupemphelerana mayina wina ndi mzake.
ZOYENERA KUDZIWA (OSAIWALA)
- Ngati muli olephera kuwerenga maphunziro a baibulo pazifukwa
zina, wina obvomelezeka kapena wophunzira bwino wapambali ayitanidwe
kutenga malo anu.
- Simuli ololedwa kupeloeka bukhu la ndondomeko yolondolera kwa
membala wina wa mkalasi lanu.
Azimayi Kupatsidwa Mphamvu
|