home >>stonecroft>>
Stonecroft- Chichewa
BUKHU LA M’MANJA LAZIPHUNZITSO ZAM’BAIBULO
LA STONECROFT AFRICA
Welcome to the Africa Stonecroft Bible Studies information E-Handbook. Extracts have been taken, with permission, from the Stonecroft website to create this unique African manual to assist with the training of the African Stonecroft Guides in places like Malawi. Some cultural adaptations have been made to suit the social climate of Africa.
CHOLINGA CHA STONECROFT NDIMASOMPHENYA AWO
Cholinga cha stonecroft ndi utumiki wawo ndi kutengela ndikulimbikitsa
azimayi kuti afikile madela awo ndi uthenga wa Yesu Khristu ndi
kulemekeza Ambuye Yesu Khristu, ndi kumupanga Ambuye Yesu kudziwika
polalika uthenga wa chipul;umutso wa M’baibolo
MASOMPHENYA AWO:
Masompheya a utumiki wa Stonecroft ndikupeleka utsogoleri wapadziko
lonse pofikila azimayi ndi Yesu Khristu.
A Stonecroft ndi utumiki wawo amasula azimayi ndi kuwalimbikisa
kuti amuziwe Yesu Khristu kwa ena
Kulalikira ndiye gwero lathu. Mongatso kwa utumiki wina uliwonse
ndi choncho. Khumbo lathu ndikufikila mzimayi wamsinkhu uliwonse
ndi nkhope iliyose ndi uthenga wa Yesu Khristu.
Pemphero ndi maziko ndi nkanamila ya china chili chose timachichita.
Yesu anati “ kopanda ine simungathe kuchita chilichose “
Jonane 15:5
Kudalila mulungu kufuna chitsogozo chake, ndiponso mdalitso wake
ndichofunika zedi.
Utumwi ndi gawo la dongosolo la utumiki wa uthenga wabwino. Momwe
azimayi akukhalira ukristu wake, moti tikupeleka mwayi ndi zipangizo
kuthandiza iwo kukula muchikhulupiliro ndiye keneko iwonnso atengele
anzawo kuchiyanjano ndi khristu.
Kusula azimayindi utsogoleri ndicholinga chathu china chautumiki
wanthu. Kuthandiza azimayi kuzindikila ndi kukulitsa mphatso zomwe
mulungu wawapatsa. Kuwazika kuti akhale atsogoleri oyenera omwe
angasinthe pakhomo, Mudzi dela dziko lawo, nditso dziko lonse kwa
Yesu Khristu.
Zolinga zaziphunzitso zabaibulo za Stonecroft ndizo kulalikila
ndi utumwi ziphunzitso zosavuta kulondolazo zammamagulu aang’ono
ang’ono zimalimbikitsa moyo wauzimu kuti akule kwa nkhala
kale zokhulupilika komano omwe akuphunzila baibolo kumene.
A Stonecroft amagawa uthenga wabwino kwa amayi padzikolonse, ozipeleka
oposa 25, 00 osulidwa bwino, nthawi ndi nthawi amayitanila azimayi
mdera awo kuti ayambe ubale wawo nd Mulungu wadzikolonse kuzela
mwa mwana wake Yesu Khristu.
Wozipeleka mudziko la United States ndiwo mayiko opyola makumi
atatu (30) amagwilitsa ntchito zipangizo zofikila za Stone craft
ndinso ziphunzitso za baibulo kugawa uthenga wabwino kwa zaka zoposela
(75) azimayi a Stonecraft adalira pemphelo ngati chida chotukulila
utumiki.
Stonecraft nd bungwe lapadziko lonse, lopanda kuyimila mpingo,
ndipotso lopanda zopindula kuchuma.
Mbiri ya Stonecroft
|