home >>stonecroft>>zofunikila >> ndondomeko yolondolera
NDONDOMEKO YOLONDOLERA
NDONDOMEKO YOLONDOLERA
CHOLINGA:
Kufikira mdera:ziphunzitso zimapeleka njira yabwino yogawana chipulumutso
ndi ena mwa Yesu Khrisu.
Tikuyang’ana zopititsa patsogoloziphunzitso za mubabaibulo
kudzera mu mipingo kuyambira mu African Bible Training School (ABTS)
KU Tanzania Malawi ndi Zambia ngakhalenso Hope Community Centre,
Kampala, Uganda.
The Pastor will identify a Church Guide,
trained to lead a Bible Study group, who will start by going through
the Stonecroft Bible Study Outreach Trinity Series starting with
‘What is God Like? then ‘Who is Jesus’ and lastly
“Where is the Holy Spirit?”
On completing the Trinity Series they will be encouraged to become
Guides, using this Handbook enabling will enable them to start a
Stonecroft Bible Study Outreach Group in their homes or local communities.
Pomaliza azalimbikitsidwa pokhala olondolera, pogwiritsa ntchito
chionetsero cha ophunzira a mu Africa ngati mbali yao ya chiphunzitso,
ngakhalenso bukhu limeneli, kuwapatsa mwayi woyambitsa phunziro
la mubaibulo mmadera awo akamabwelera mmamidzi mwao, poitanitsa
anzawo, mabanja, ogwira nawo ntchito ndi anansi awo.
Utumiki. A khristu atsopano ndi okhwima monga azibutsa pa (ATBS)atja
kuphunzira zambiri za mulungu ndikukula mu chiyanjano ndi Iye. Ziphunzitso
zimafotokozera za momwe tingaikile mfundo za mbaibulo m’moyo
wathu wa tsiku ndi tsiku.
UPADERA
Ndiye chomwe chimapangitsa ziphunzitso za mu baibulo za Stonecroft
kusiyana ndi ziphunzitso zina zopezeka pa msika nchiyni?
• The studies are designed to be used
with a New Testament however the page numbers have been removed
in the Chichewi translation of the Bible Study and a Bible Verse
Handbook has been created in cases where the participants do not
have a Bible of their own.
• Ziphunzitso zimapangidwa ntchito chipangano chatsopano chomwe
chili chopezekelatu kudzera ku bungwe la ma baibulo la Tanzania,
cholinga chawo ndikufalitsa uthenga wabwino wa Yesu Khristu ndikulimbikitsa
malembo kwa anthu m’moyo wawo wa tsiku ndi tsiku bukhu la
mgwirizano wa tsopano mchilankhulo cha chiswahili ndilopezeka ku
bungwe la ma baibulo lopezeka mkati mwa Tanzania mdera la Dodoma.
Masamba ena atanthauzilidwa mu chiswahili chophunzitsa baibulo kugwirizana
ndi Kamasulidwe ka umodzi (union verson)
• Ziphunzitso zalembedwa mwandondomeko yotsatidwa bwino kwa
omwwe ndi oyamba kumene kuphunzira baibulo.
• Kumbukirani kuti ndondomeko yolondolera baibulo simphunzitsi
koma ndikuphunzira limodzi ndi omwe akuchita nawoziphunzitso za
baibulo.
NDONDOMEKO ZABWINO
Ziphunzijtso za baibulo za Stonecroft sizobvuta kuwenga
Zoyenera kudziwa olondolera zoikida mmadontho a malire a bukhu
lolondolera. Izi nzoyenera kuwerengedwa mokwweza kwa onse otenga
nawo gawo.
Madontho angapo (……….) akusonyeza kuti olondolera
ayenela kulola gulu kutenga nawo mbali poyankha mafunso, kuwerenga
nawo vesi la mu baibulo mwina kueleka mfundo pa mutu omwe ukukambidwawo.
Zilembo zotsindikizidwa mowonjezera ndikusonyezedwa mu baibulo
motsatana ndi madontho asanu zikuwonjeza vesi lomwe liyenera kuwerengedwa
mokweza pa nthawi ya ziphunzitso ndi mmodi wagululo.
Ngati mosonyezera zili motsindikizidwa mwanthawi zones, zikusonyeza
kuti nzotalikitsidwa kwambiri kuziwernga pagulu kapena sizofuna
kupeza yankho lake.
Kutsogolera kalasi
|