Project Hope     home >>stonecroft >>ndondomeko ya kuphunzila>>zofunikila
Stonecroft
Women's Empowerment Program
Sports Bible Club
Living Water Bible Club

ZOFUNIKILA ABUSA KAPENA NGWILIZANITSI

  • Alandile folam yakutha yofunsila kuchokela kwa woyenera kulondolera
  • Alondole moyenela mkuwerenga folum yofunsila kuti atenge chitsimikizo choti umboni wa wolondolera ndi omveka bwino.
  • Mwapephero muyenela kumufutsa mafutso angapo wokhuza chiyanjano chake ndi Yesu Hhristu mwana wa Mlungu monga:-
    (1) Ndikufuna kuzwa za ulendo wako ndi mulungu, Khristu kodi wagwilapo gawo lanji?
    (2) Ngati wotenga mbali pa ziphunzitso za baibulio za Srtonecroft atakufutsa zamomwe ungakhalire pa chiyanjano ndi Mulungu inu mungamuyankhe motani?
    (3) Mukuwumvetsa bwanji uthenga wabwino, ndipo mungaulumikizitse motani
    (4) Mungathe guganizila kuwerengapo mabuku la Mungathe kuchikhulupila? Ndi olondolerayo.
  • Funani nthawi yolumikizana ndiolondolerayo gwilitsani tchito zida izi
    (1) Bukhu lamanja la African Stonecroft ziphunzitso za m’baibulo.
    (2) Ndondomeko polondolera patsogolo pa bukhu la la dongotsolo ngati sanayambe achitapo phunzilo la Stonecroft muyenela kugwila ntchito limozi muziphunzitso zochepelapo mukabuku ka Yesu ndi ndani? Kuti amvese zomwe zili nkati.

Abutsa kapena olumikizitsa asunge chikalata chofunsila mumabukhu awo.

Kumbukani kuti sionse ali wokonzeka kukhala wolondolera ngati mwaziwisana kuti wian wake Sali woyenera kukhala wolondolera posasata masomphenya eni eni a zophunzitsa m’baibulo za Stonecroft mupewe zokangana za kuthupi pena zandale mungomutengera mwabwino kumusiyitsa kulondolera mwa njira ina mumutenge kukhala mmodzi wotenga nawo mbali ya kuphunzila nawo ziphunzitso za Baibulo, muyenela kukambilana izi ndi mtsogoleri wankulu kapena m’butsa wake.

Mukamaliza ntchito yophunzitsa wolondolerawo mulumikizane ndi mulangizi wankulu pa makina a intanet kwa African Stonecroft wamdela lanulo kuti mutengetso ndondomeko ina yolondola

Wamkulu wamuderalanulo azalumikizana ndi a stonecroft utumiki wothandiza waku America pa mfundoyi atha kupanga zimenezi polemba pamakina a internet ku connections@stoncroft.org

Chone musayiwale za olondolera address yake ndi nambala ya lamya nditso addrees yapamakina a internrt monga momwe mwatiwonela pankhani ya ndondomeko ya kaphunzitsidwe ka Baibulo

Pomwe a Stonecroft azalandile uthengawu osankhidwa watsopano wolondolerayo azalandila pamakina a internet kulandilidwa jkwake komwe kuzatanthauzidwile mchilankhulo cha kudera lakelo kumuziwitsa za udindo wake watsopanowo , olondolera azakhalatso gawo lamulumikizano wa odzipeleka ndipo athatso kulandila nyuzi pepala ya Stonecroft ya chingerezindikuthekelatso kulu ndi atsogoleri pa makina a internet zokhuzana ndi utumiki wa Stonecroft.

Kudziwitsa za olondolerawo kutha kusimikidzila za kuziwika kwawo ngbati atsogoleri, timamuyika munthu aliyense wokhunzika muutumiki wofunikila kwambiri ndipo ngati mbali yofikilitsa ziko lathu kwa Yesu Khristu.

KUSULA BWINO WOLONDOLERA WA STONECROFT

Wolondolera wophunzitsidwa bwino ndiwofunikila kwambili paukafdaulo wa anthu okumba chikhulupiliro nditso omwe akhala muziphunzitso za baibulo kwa zaka zambiri.

Agwirizanitsi ambiri amalemba ma nyuzi pepala kwa nthawi ndi nthawipofuna kulumikizana nawo, mikumano yoitanitsa, ngati ili yopezeka pa SKYPE, olo njira zina zamakina a internet ndikuthekela kwina kofuna kolumumikizana ndi olondolera a mdela lanu.

Agwirizanitsi ayenera kupanga ndiondomeko pa kanthawi pachaka yoti kulumikizana ndi olondolera powayamikira mowathandizila ndi chilimbikitso ngakhale kuwakhazikitsa momwe angayendetsele bwinon ziphunzitso zamubaibulo za Stonecroft.

Zambiri zimachitika zothandiza kuleza mkulumikizana, pemphero, kugawana zofuna zanu ndinso kuphunzira luso lina, ndikudziwa momwe angayankhile mafunso ovuta

Nthawi yophunzitsa olondolera itha kukonzedwa pachaka ngati pokumana kwa Khirisimisi olo mwina zosangalatso ngati tsiku lokumbukira kubadwa mwinanso tchuti kumene chapadera.

Izi ndi zina zoganizilapo pakasankhidwe ka nthawi yophunzitsira olondolera
• Nthawi yapadela ya mapemphero ndi chiyanjano
• Nthawi yopikkisana za malembo, pemphero lapadela lodzipeleka, poyamika ndikulimbikitsa olondolera potumikila.
• Pokhazikita olondolera ena ndipogawana zotsatila zabwino pamaphunziro awo

Ntawi yabwino ngati ugawidwe wa umboni, kuchulukitsa utumiki mdera lanu, kukhazikitsa utumiki wa Stonecroft kwa mpingio mdela lanu olo bungwe lochita chita mdera lanulo. Iyi itha kukhalanso nthawi yophunzira kwa wina ndi mzake. Mulore olondolera agawane momwe amaitanila otenga nawo mbali, nthawi yobvuta yomwe akumana nayo, ndi pomwe amuona Mulungu akuchita ntchto yyake mwa otenga nawo mbali (m’moyo wawo).

Mumalize nd chilimbikitso ndikupemphelerana wina ndi mzake

Ndondomeko Yolondolera
 
 

 

 
 
Copyright ©  2023 www.UnitedCaribbean.com. All rights reserved. Disclaimer Click to Contact us