home >>stonecroft>>mbili ya stonecroft>>utsogoleri
wawo wa stonecroft
UTSOGOLERI WAWO WA STONECROFT
UTSOGOLERI WAWO WA STONECROFT
Astsogoleri a Stonecraft amagawana nawo maudindo ndi kalongosoledwe
ka zochitika za siku ndi siku ku maofesi aakulu ndi mmadela ena.
DR NAOMI CRAMER OVERTON (President ndi Bwana wamukulu)
Dr. Naomi Cramer Overton, Doctor of Intercultural
Studies from Fuller Theological Seminary, researched nearly 30,000
families to develop a model to move faith communities and families
to give, serve and grow in their compassion and character. She served
as president and CEO of MOPS (Mothers of Preschoolers) International,
she holds an MBA from UCLA and a degree related to culture, poverty,
and communications from Stanford University. She is now the President
and CEO of Stonecroft.
DORIS THOMPSON – (Vice President
of Transformation)
Doris Thompson amathandiza azimayi kuyika masomphenya awo ndi maganizo
awo mukuchitachita ngati wachiwiri kwa president wa utumiki wofikila
mmadela iwowo a Doris zolinga zawo ndikufikila azimayi ochuluka
mmadela ochuluka ndikuthekela kwa njira zonse. Amagwira ntchito
kutukula mautumiki ofikila mmadela ndikukhazikitsa odzipeleka a
Stonecraft kubzyala madela ena awutumiki.
Alipo azikulu akulu ena ammaudindo ndi gulu la utsogoleri amene
ambiri aiwo simungayenele kulumikizana nawo
Stonecroft utumiki wawo ndiwokhumbitsitsa kukulumikizanitsani azimayi
kwa wina ndi mzake ndi madera ena ndi anzake
A Stonecroft amalimbikitsa azimayi kupeza njira zothekela kupanga
kulumikizana ndi azawo m’madera ndikuyitanila kumaphunziro
a baibulo a mtsogolomu mudera kapena mzinda wawo
Ndi osavuta kusatawa aziphunzitsozi amadzetsa mupweya wabwino wa
uzimu kwa okhulupilira akale komatso alendo ndi baibulo.
Utumiki wa Stonecroft umamva ndi kuyamikila zofunikila m’zimayi
ndi Khristu, mumakhuza aliyense mudela lake , mwamuna wake, ana
anzake anasi ndi ogwira naye ntchito limodzi.
Ndemanga Ya Chikhulupiriro
|