home >>stonecroft>>azimayi
kupatsidwa mphamvu >> utumiki wachi afrika
CHITSANZO CHABWINO CHA UTUMIKI WACHI AFRIKA
CHITSANZO CHABWINO CHA UTUMIKI WACHI AFRIKA
Utumwi wachitsanzo wachifilika watsimikiza kuti nkwabwino kugawa
kuti muchulukitse ndinso kuchulukitsa nkwabwino kuposa kuonjezeera
1. Chitsanzochi chamu Africa chiidzayambitsidwa kaye poyamba mu
Tanzania kudzera ku (ATBS) cholinga chake chenicheni ndikuphunzitsa
a Stonecraft ziphunzitso za mu baibulo kwa olondolera. Pogwiritsa
ntchito kanema wa ziphunzitso ndinso bukhu la olondolera lamanja
la ziphunzitso, tidzapatsa chitysogozo kwa azibusa omwe akupanga
nawo maphunziro awo tsopanowa pa (ATBS) ku Tanzania komanso Malawi
ndi Zambia. Azibusa amenewa adzakhala oondolera oyamba mu Tanzania
Mulungu akalolra. Adzapatsidwa aliyense limodzi mwa ma baibulo la
mgwirizano swahiri chipangano chatsopano, limodzi la bukhu lawolondolera
ndi ndongosolo lakle ndi mabaibulo a ziphunzitso zowelenga mu ndime
ya utatu woyera, mkamaka khumi a Yesu ndiye ndani? Kenako khumi
a Mulungu ali ngati chiyani? Ndilotsiriza lake la kodi Mzimu woyera
ali kuti? Khumi nawo.
2. Azibusa adzaqtengera uthengau ku mipingo yawo kumadela kwawoko
ndikupeza mzimayi wachangu pa ntchito ya mulungu kaya ndimtsogoleri
wa azimayi, pogwiritsa ntchito kanema yophunzitsirayo ndi bukhu
la wolondolera la Stonecroft mu Africa la mmanja, adzaphunzitsa
olondolera m’mipingo wamba yoyambira kwawoko, ndiye m’usayo
mgwirizanitsi woyang’anira mayiyo
3. Wolondoler watsopano adzapatsidwa mabaibulo atsopano khumi achipangano
chatsopano, bukhu la wolondolera mwadongosolo la Stonecraft, ndi
khumi la mabukhu ophunzira baibulo a Stonecraft a kodi Yesu ndi
ndani? Onse otanthauzilidwa mu chiphunzitso cha kwawo chomwe ndipo,
adzafuna amayi asanu a mum’pingo momwemo oyenera kulondolera
bwino kuti ayambe kutenga gawo. Mmodzi mwa amayi olondolera osankhidwawoatha
kubweretsa mzawo m’modzi, makamaka opemphera naye ku gulu
laziphunzitso za baibulo, ngati ziphunzitso za baibulo zatha adzaphunzitsa
azimayi asanu osankhidwawo kuti akhale gawo achitatu la wolondolera
a Stonecraft mogwiritsa ntchito kanema wophunzitsilayo ndimabukhu
ophunzitsilayo ndi mabukhu ophunzilira ophunzilira baibulo a Stonecroft
a m’manja
4. Adzakhala mgwirizanitsi kuwonelera olondolera asanuwo
5. M’usa adzakhala mgwirizanitsi wankulu woonelera ntchitozo.
6. M’modzi wa olondolera asanuwo pamodzi ndi anzawo opemphera
nawowo adzapeza muntu wachangu m’modzi kuchoka pa mpingo wawo
mwina mdelaro ndi winanso woyenera woti atha kulondolera bwino kuchoka
ku mpingo wina mopmvana ndi abusa ake kumuloleza.
7. Pamodzi amayi anayiwa adzalimbikitsa anthu omwe Sali okhulupilira
kulowa mgulu ophunzira atsopanowa anthu awiri aliyense. Kumbukani
maphunziro a baibulowa ayenenera kusapitilira anthu okwana khumi.
8. Ngati ziphunzitso za baibulo za Yesu ndiye ndani? Zatheka ayenera
kuphunzitsa amayi awiriwo (m’modzi wochoka kumpingo wake winayo
ku mpingo wina) kuti adzakhale gulu lachinayi la wolondolera a Stonecroft.
Wopemphera naye mzakeyo adzakhala naye kuphunzitsa mkalasi kuphunszitsa
ziphunzitso zina za baibulo za muphunziro la utatu woyera.
9. Dongosololi limatsatidwanso ku mipingo ina yomwe yaikidwa nawo
mu ndondomeko imeneyi
10. Ngati pali mafunso ena onse amene olondolera sangathe kuyankha
ayenela kuwapeleka kwa mgwirizanitsi amene ayenera kukhal mbusa.
11. Pomwe nthawi ikupita agwirizanitsi ena adzakhala akuphunzitsa
ngati mgwirizano ukukula kanema adzakhala akugwiritsidwa ntchito
kwa ziphunzitso za wogwirizanitsa
12. Kumbukirani kugawa kugawa kuti muchulukitse.
13. Kuchulukitsa nkwabwino kuposa kuwonjezera
“muyenera kukhala a tcheru, kuima
njii mu chikhulupiliro, khalani olimbika, amphamvu. Muchite ntchito
zanu zones mucikondi”
1 Akorinte 16:13-14
|